Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 6:8 - Buku Lopatulika

8 Masiku onse a kusala kwake akhala wopatulikira kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Masiku onse a kusala kwake akhala wopatulikira kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Munthuyo ndi wopatulikira Chauta masiku onse a kudzipereka kwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Munthuyo ndi wopatulika masiku onse odzipereka kwake kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 6:8
5 Mawu Ofanana  

Asadzidetse ndi atate wake, kapena mai wake, mbale wake, kapena mlongo wake, akafa iwowa; popeza chowindira Mulungu wake chili pamutu pake.


Munthu akafa chikomo pali iye, ndipo akadetsa mutu wake wowinda; pamenepo azimeta mutu wake tsiku la kumyeretsa kwake, tsiku lachisanu ndi chiwiri aumete.


Ndinampempha mwanayu; ndipo Yehova anandipatsa chopempha changa ndinachipempha kwa Iye;


chifukwa chake inenso ndinampereka kwa Yehova; masiku onse a moyo wake aperekedwa kwa Yehova. Ndipo analambira Yehova pomwepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa