Numeri 6:6 - Buku Lopatulika6 Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 “Masiku onse pamene munthuyo wadzipereka kwa Chauta, asayandikire mtembo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pa nthawi yonse imene munthuyo wadzipatula yekha kwa Yehova asayandikire mtembo. Onani mutuwo |