Numeri 6:4 - Buku Lopatulika4 Masiku onse a kusala kwake asadye kanthu kopangika ndi mphesa, kuyambira nthanga zake kufikira khungu lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Masiku onse a kusala kwake asadye kanthu kopangika ndi mphesa, kuyambira nthanga zake kufikira khungu lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Masiku onse pamene munthuyo ali wodzipereka kwa Chauta, asadye chilichonse chochokera ku mphesa, ngakhale mbeu zake kapena makungu ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pa nthawi yonse imene ali Mnaziri, asamadye chilichonse chopangidwa kuchokera ku mphesa ngakhale mbewu zake kapena makungu ake.’ Onani mutuwo |