Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 6:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo chilamulo cha Mnaziri, atatha masiku a kusala kwake ndi ichi: azidza naye ku khomo la chihema chokomanako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo chilamulo cha Mnaziri, atatha masiku a kusala kwake ndi ichi: azidza naye ku khomo la chihema chokomanako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 “Lamulo la Mnaziri pamene nthaŵi ya kudzipereka kwake yatha, nali: abwere naye pakhomo pa chihema chamsonkhano,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 “Tsono ili ndi lamulo la Mnaziri pamene nthawi yodzipatula kwake yatha: Abwere naye pa khomo la tenti ya msonkhano.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 6:13
4 Mawu Ofanana  

Ndipo awapatulire Yehova masiku a kusala kwake, nadze nayo nkhosa yamphongo ya chaka chimodzi ikhale nsembe yopalamula; koma masiku adapitawa azikhala chabe, popeza anadetsa kusala kwake.


Chifukwa chake uchite ichi tikuuza iwe; tili nao amuna anai amene anawinda;


Pamenepo Paulo anatenga anthuwo, ndipo m'mawa mwake m'mene anadziyeretsa nao pamodzi, analowa mu Kachisi, nauza chimalizidwe cha masiku a kuyeretsa, kufikira adawaperekera iwo onse mtulo.


Ndipo pamene masiku asanu ndi awiri anati amalizidwe, Ayuda a ku Asiya pomuona iye mu Kachisi, anautsa khamu lonse la anthu, namgwira,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa