Numeri 5:29 - Buku Lopatulika29 Ichi ndi chilamulo cha nsanje, pamene mkazi, pokhala naye mwamuna wake, ampatukira nadetsedwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ichi ndi chilamulo cha nsanje, pamene mkazi, pokhala naye mwamuna wake, ampatukira nadetsedwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 “Limeneli ndilo lamulo la za nsanje, pamene mkazi azembera mwamuna wake, nadziipitsa, ngakhale kuti ali m'manja mwa mwamuna wakeyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 “ ‘Limeneli ndiye lamulo la nsanje pamene mkazi wayenda njira yoyipa ndi kudzidetsa ali pa ukwati ndi mwamuna wake, Onani mutuwo |