Numeri 5:28 - Buku Lopatulika28 Koma ngati mkazi sanadetsedwe, nakhala woyera, pamenepo adzapulumuka, nadzaima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Koma ngati mkazi sanadetsedwe, nakhala woyera, pamenepo adzapulumuka, nadzaima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Koma mkaziyo akakhala kuti sadadziipitse ndipo alibe tchimo, adzakhala wopanda mlandu, ndipo azidzabala ana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Koma ngati mkaziyo sanadzidetse ndi kuti alibe tchimo, adzakhala wopanda mlandu ndipo adzabereka ana. Onani mutuwo |