Numeri 4:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo atenge nsalu yamadzi, ndi kuphimba choikaponyali younikira, ndi nyali zake, ndi mbano zake, ndi zoolera zake, ndi zotengera zake zonse za mafuta zogwira nazo ntchito yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo atenge nsalu yamadzi, ndi kuphimba choikapo nyali younikira, ndi nyali zake, ndi mbano zake, ndi zoolera zake, ndi zotengera zake zonse za mafuta zogwira nazo ntchito yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Atenge nsalu yobiriŵira ndi kuphimba choikaponyale, pamodzi ndi nyale zake, mbaniro zake, mbale za phulusa ndi ziŵiya zake zonse za mafuta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Azitenga nsalu ya mtundu wa thambo ndi kukutira choyikapo nyale, pamodzi ndi nyale zake, zopanira zake, zotengera zake ndi mitsuko yonse yosungiramo mafuta. Onani mutuwo |