Numeri 4:45 - Buku Lopatulika45 Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Ameneŵa ndiwo anthu a m'mabanja a Merari, anthu amene Mose ndi Aroni adaŵaŵerenga, monga momwe Chauta adaalamulira kudzera mwa Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Ichi ndicho chinali chiwerengero cha mabanja a Amerari. Mose ndi Aaroni anawawerenga monga momwe Yehova anawalamulira kudzera mwa Mose. Onani mutuwo |