Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:46 - Buku Lopatulika

46 Owerengedwa onse a Alevi, amene Mose ndi Aroni ndi akalonga a Israele anawawerengera, monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Owerengedwa onse a Alevi, amene Mose ndi Aroni ndi akalonga a Israele anawawerengera, monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Choncho Mose ndi Aroni, pamodzi ndi atsogoleri a Aisraele, adaŵaŵerenga Alevi onsewo potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Kotero Mose, Aaroni ndi atsogoleri a Israeli anawerenga Alevi onse monga mwa mafuko ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:46
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anawerengedwa Alevi oyambira zaka makumi atatu ndi mphambu, ndipo chiwerengo chao kuwawerenga mmodzimmodzi ndicho amuna zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu.


ndi iwo oyesedwa mwa chibadwidwe cha ansembe mwa nyumba za makolo ao, ndi Alevi, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu mu udikiro mwao, monga mwa zigawo zao;


Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose.


kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa kugwira ntchito ya utumikiwu, ndiyo ntchito ya akatundu m'chihema chokomanako;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa