Numeri 4:43 - Buku Lopatulika43 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 kuyambira anthu a zaka makumi atatu mpaka a zaka makumi asanu, onse amene ankatha kutumikira m'chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Amuna onse kuyambira zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzatumikira ntchito mu tenti ya msonkhano, Onani mutuwo |