Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 4:43 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Amuna onse kuyambira zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzatumikira ntchito mu tenti ya msonkhano,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

43 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 kuyambira anthu a zaka makumi atatu mpaka a zaka makumi asanu, onse amene ankatha kutumikira m'chihema chamsonkhano.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:43
5 Mawu Ofanana  

Aamuna onse a zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano,


Amerari anawawerenga monga mwa mafuko ndi mabanja awo.


atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 3,200.


“Ntchito za Alevi ndi izi: Amuna a zaka 24 kapena kuposera pamenepa ndiye azibwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano.


Ndipo Yesu anali ndi zaka makumi atatu pamene anayamba ntchito yake. Monga mmene anthu ankaganizira, Iyeyo anali mwana wa Yosefe, mwana wa Heli,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa