Numeri 4:40 - Buku Lopatulika40 owerengedwa ao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi limodzi kudza makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 owerengedwa ao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi limodzi kudza makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Chiŵerengero chao chidakwanira 2,630 potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 2,630. Onani mutuwo |