Numeri 4:39 - Buku Lopatulika39 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 kuyambira anthu a zaka makumi atatu mpaka makumi asanu, onse amene ankatha kutumikira m'chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Amuna onse a zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano, Onani mutuwo |