Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:38 - Buku Lopatulika

38 Ndipo ana owerengedwa a Geresoni, monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

38 Ndipo ana owerengedwa a Geresoni, monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

38 Adaŵerenganso ana a Geresoni potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

38 Ageresoni anawerengedwanso monga mwa mafuko ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:38
4 Mawu Ofanana  

ndi iwo oyesedwa mwa chibadwidwe cha ansembe mwa nyumba za makolo ao, ndi Alevi, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu mu udikiro mwao, monga mwa zigawo zao;


Owerengedwa ao, powawerenga amuna onse, kuyambira mwana wa mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao ndiwo zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.


Awa ndi owerengedwa a mabanja a Akohati, onse akutumikira m'chihema chokomanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose.


kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa