Numeri 4:36 - Buku Lopatulika36 ndipo owerengedwa ao monga mwa mabanja ao ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndipo owerengedwa ao monga mwa mabanja ao ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 ndipo chiŵerengero chao chidakwanira 2,750 potsata mabanja ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 atawawerenga mwa mafuko awo, anali 2,750. Onani mutuwo |