Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:34 - Buku Lopatulika

34 Ndipo Mose ndi Aroni ndi akalonga a khamu anawerenga ana a Akohati monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo Mose ndi Aroni ndi akalonga a khamu anawerenga ana a Akohati monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Tsono Mose ndi Aroni, pamodzi ndi atsogoleri a mpingo, adaŵerenga ana a Akohati potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Mose, Aaroni ndi atsogoleri a magulu a anthu anawerenga Akohati monga mwa mafuko ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:34
5 Mawu Ofanana  

Awa ndi ana a Levi monga mwa nyumba za makolo ao, ndiwo akulu a nyumba za makolo a iwo owerengedwa mwa chiwerengero cha maina mmodzimmodzi, akugwira ntchito ya utumiki wa nyumba ya Yehova, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu.


Ndipo pamodzi ndi inu pakhale munthu mmodzi wa mafuko onse; yense mkulu wa nyumba ya kholo lake.


Banja la Aamuramu, ndi banja la Aizihara, ndi banja la Ahebroni, ndi banja la Auziyele ndiwo a Kohati; ndiwo mabanja a Akohati.


Iyi ndi ntchito ya mabanja a ana a Merari, monga mwa ntchito zao zonse m'chihema chokomanako, mowauza Itamara mwana wa Aroni wansembe.


kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa