Numeri 4:33 - Buku Lopatulika33 Iyi ndi ntchito ya mabanja a ana a Merari, monga mwa ntchito zao zonse m'chihema chokomanako, mowauza Itamara mwana wa Aroni wansembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Iyi ndi ntchito ya mabanja a ana a Merari, monga mwa ntchito zao zonse m'chihema chokomanako, mowauza Itamara mwana wa Aroni wansembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Imeneyi ndiyo ntchito ya mabanja a ana a Merari, ndipo ntchito yao yonse ya m'chihema chamsonkhanoyo, aziiyang'anira ndi Itamara, mwana wa wansembe Aroni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Iyi ndiyo ntchito ya mafuko a Amerari pamene akugwira ntchito ku tenti ya msonkhano motsogozedwa ndi Itamara mwana wa wansembe Aaroni.” Onani mutuwo |