Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Yehova anawuzanso Mose ndi Aaroni kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:17
2 Mawu Ofanana  

Ndipo zoyang'anira Eleazara, mwana wa Aroni wansembe, ndizo mafuta a nyaliyo, ndi chofukiza cha fungo lokoma, ndi nsembe yaufa kosalekeza, ndi mafuta odzoza, udikiro wa chihema chonse, ndi zonse zili m'mwemo, malo opatulika, ndi zipangizo zake.


Musamasadza fuko la mabanja a Akohati kuwachotsa pakati pa Alevi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa