Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 4:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo azichotsa mapulusa paguwa la nsembe, ndi kuyala pa ilo nsalu yofiirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo azichotsa mapulusa pa guwa la nsembe, ndi kuyala pa ilo nsalu yofiirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ataye phulusa lapaguwa, ndipo ayalepo nsalu yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 “Azichotsa phulusa la pa guwa lansembe lamkuwa ndi kuyalapo nsalu yapepo pamwamba pake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:13
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anaomba zovala zakutumikira nazo ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, atumikire nazo m'malo opatulika, naomba zovala zopatulika za Aroni; monga Yehova adamuuza Mose.


zovala zokoma za kutumikira nazo m'malo opatulika, ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zovala za ana ake, kuchita nazo ntchito ya nsembe.


Naikepo zipangizo zake zonse, zimene atumikira nazo pamenepo, mbale za zofukiza, mitungo, ndi zoolera, ndi mbale zowazira, zipangizo zonse za guwa la nsembe; nayalepo chophimba cha zikopa za akatumbu, ndi kupisako mphiko zake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa