Numeri 36:6 - Buku Lopatulika6 Cholamulira Yehova za ana aakazi a Zelofehadi ndi ichi, kuti, Akwatibwe nao amene afuna eni ake; komatu akwatibwe nao a banja la fuko la makolo ao okhaokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Cholamulira Yehova za ana akazi a Zelofehadi ndi ichi, kuti, Akwatibwe nao amene afuna eni ake; komatu akwatibwe nao a banja la fuko la makolo ao okhaokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Zomwe Chauta akulamula za ana aakazi a Zelofehadi ndi izi: Aloleni akwatiwe ndi yemwe akumufuna, malinga akwatiwe ndi a m'banja la fuko la makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Izi ndi zimene Yehova akulamula kwa ana aakazi a Zelofehadi: Atha kukwatiwa ndi aliyense amene angakondweretsedwe naye koma zingakhale bwino atakwatiwa mʼfuko la abambo awo Onani mutuwo |