Numeri 36:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Mose analamulira ana a Israele monga mwa mau a Yehova, nati, Fuko la ana a Yosefe linena zoona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Mose analamulira ana a Israele monga mwa mau a Yehova, nati, Fuko la ana a Yosefe linena zoona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamenepo Mose adaŵalamula Aisraele potsata mau a Chauta, adati, “Zimene akunena ana a Yosefezi nzoona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsono mwa lamulo la Yehova, Mose anapereka lamulo ili kwa Aisraeli: “Zimene ana a Yosefe akunena ndi zoona. Onani mutuwo |