Numeri 36:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pofika chaka choliza cha ana a Israele adzaphatikiza cholowa chao ku cholowa cha fuko limene akhalako; chotero adzachotsa cholowa chao ku cholowa cha fuko la makolo athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pofika chaka choliza cha ana a Israele adzaphatikiza cholowa chao ku cholowa cha fuko limene akhalako; chotero adzachotsa cholowa chao ku cholowa cha fuko la makolo athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndipo chikafika chikondwerero cha Aisraele cha chaka cha 50, choloŵa chaocho chidzaonjezedwa pa choloŵa cha fuko la amuna ao. Motero choloŵa chao chidzachotsedwa pa choloŵa cha fuko la makolo athu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pamene chaka cha chikondwerero cha zaka makumi asanu, cha Aisraeli chafika, cholowa chawo chidzawonjezeredwa ku fuko limene iwo akwatiwako. Ndipo katundu wawo adzachotsedwa pa cholowa cha fuko la makolo athu.” Onani mutuwo |