Numeri 36:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo akakwatibwa nao ana aamuna a mafuko ena a ana a Israele, achichotse cholowa chao ku cholowa cha makolo athu, nachionjeze ku cholowa cha fuko limene adzakhalako; chotero achichotse ku maere a cholowa chathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo akakwatibwa nao ana amuna a mafuko ena a ana a Israele, achichotse cholowa chao ku cholowa cha makolo athu, nachionjeze ku cholowa cha fuko limene adzakhalako; chotero achichotse ku maere a cholowa chathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma ngati akwatiwa ndi amuna a mafuko ena a Aisraele, choloŵa chao chidzachotsedwa pa choloŵa cha makolo athu ndi kuwonjezera pa choloŵa cha fuko la amuna aowo, motero choloŵa chathu chidzachepa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsopano ngati akwatiwa ndi aamuna ochokera ku mafuko ena a mitundu ya Aisraeli, cholowa chawo chidzatengedwa kuchoka pa cholowa cha makolo athu ndipo adzachiwonjezera ku fuko limene akwatiwakolo. Ndipo gawo lina la cholowacho, lopatsidwa kwa ife lidzatengedwa. Onani mutuwo |