Numeri 36:11 - Buku Lopatulika11 popeza Mala, Tiriza, ndi Hogila, ndi Milika, ndi Nowa, ana aakazi a Zelofehadi, anakwatibwa ndi ana aamuna a abale a atate wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 popeza Mala, Tiriza, ndi Hogila, ndi Milika, ndi Nowa, ana akazi a Zelofehadi, anakwatibwa ndi ana amuna a abale a atate wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mala, Tiriza, Hogola, Milika ndi Nowa, ana aakazi a Zelofehadi, adakwatiwa ndi ana a abale a bambo wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ana aakazi a Zelofehadi amene ndi Mahila, Tiriza, Hogila, Milika ndi Nowa, anakwatiwa ndi asuweni awo a ku mbali ya abambo awo. Onani mutuwo |