Numeri 35:7 - Buku Lopatulika7 Midzi yonse muipereke kwa Alevi ndiyo mizinda makumi anai ndi isanu ndi itatu, iyo pamodzi ndi mabusa ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Midzi yonse muipereke kwa Alevi ndiyo midzi makumi anai ndi isanu ndi itatu, iyo pamodzi ndi mabusa ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mizinda imene mudzapatse Alevi idzakhale 48 yonse pamodzi, kuphatikizanso ndi mabusa ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Midzi yonse imene mudzapereke kwa Alevi idzakhale 48, pamodzi ndi malo oweterako ziweto. Onani mutuwo |