Numeri 35:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo mabusa a mizindayo, imene muipereke kwa Alevi ndiwo a mikono chikwi chimodzi kuyambira kulinga kufikira kunja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo mabusa a midziyo, imene muipereke kwa Alevi ndiwo a mikono chikwi chimodzi kuyambira kulinga kufikira kunja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mabusa a mizindayo amene mudzapatse Aleviwo, adzayambire ku khoma la mzinda, adzatuluke kunja mamita 450, kuzungulira mzindawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Malo a msipu a mudziwo amene mudzawapatse Aleviwo, adzayambire ku khoma la mudzi ndipo adzatuluke kunja mamita 450, kuzungulira mudziwo. Onani mutuwo |