Numeri 35:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mizinda ndiyo yokhalamo iwowa; ndi mabusa akhale a ng'ombe zao, ndi zoweta zao, inde nyama zao zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo midzi ndiyo yokhalamo iwowa; ndi mabusa akhale a ng'ombe zao, ndi zoweta zao, inde nyama zao zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mizindayo idzakhala yao yoti azikhalamo, ndipo mabusa ao adzakhala odyetseramo ng'ombe zao, zoŵeta zao ndi nyama zao zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Midziyo idzakhala yawo ndipo azidzakhala mʼmenemo. Malo a msipu adzakhala a ngʼombe, nkhosa ndi zoweta zawo zina zonse. Onani mutuwo |