Numeri 35:2 - Buku Lopatulika2 Uza ana a Israele, kuti apatseko Alevi cholowa chaochao, mizinda yokhalamo; muwapatsenso Alevi mabusa akuzungulira mizinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Uza ana a Israele, kuti apatseko Alevi cholowa chaochao, midzi yokhalamo; muwapatsenso Alevi mabusa akuzungulira midzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Ulamule Aisraele kuti pa choloŵa chaocho, apatseko Alevi mizinda yoti azikhalamo. Ndipo Aleviwo muŵapatsenso mabusa pozungulira mizindayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Lamula Aisraeli kuti apereke kwa Alevi midzi yoti azikhalamo kuchokera pa cholowa chomwe adzalandira. Muwapatsenso malo oweteramo ziweto kuzungulira midziyo. Onani mutuwo |
Ndi m'malire a Yuda, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo, pakhale chopereka muchipereke, mikono zikwi makumi awiri mphambu zisanu kupingasa kwake, ndi m'litali mwake lilingane ndi magawo enawo, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; ndi malo opatulika akhale pakati pake.