Numeri 34:17 - Buku Lopatulika17 Maina a amunawo adzakugawirani dziko likhale cholowa chanu, ndi awa: Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Maina a amunawo adzakugawirani dziko likhale cholowa chanu, ndi awa: Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 “Maina a anthu amene adzakugaŵireni dzikolo kuti likhale choloŵa chanu, ndi wansembe Eleazara ndi Yoswa mwana wa Nuni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Awa ndi mayina a anthu amene adzakugawireni dzikoli kuti likhale cholowa chanu: wansembe Eliezara ndi Yoswa mwana wa Nuni. Onani mutuwo |