Numeri 34:15 - Buku Lopatulika15 mafuko awiriwa ndi hafu adalandira cholowa chao tsidya lija la Yordani ku Yeriko, kum'mawa, kotulukira dzuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 mafuko awiriwa ndi hafu adalandira cholowa chao tsidya lija la Yordani ku Yeriko, kum'mawa, kotulukira dzuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mafuko aŵiriwo ndi thekalo adalandira kale choloŵa chao patsidya pa mtsinje wa Yordani ku Yeriko chakuvuma kotulukira dzuŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mafuko awiriwa pamodzi ndi theka la fuko la Manase analandiriratu cholowa chawo patsidya pa mtsinje wa Yorodani ku Yeriko cha kummawa kotulukira dzuwa.” Onani mutuwo |