Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo anachokera ku Etamu, nayenda nabwerera ku Pihahiroti, ndiko kutsogolo kwake kwa Baala-Zefoni; namanga iwo patsogolo pa Migidoli.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo anachokera ku Etamu, nayenda nabwerera ku Pihahiroti, ndiko kutsogolo kwake kwa Baala-Zefoni; namanga iwo patsogolo pa Migidoli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Adanyamuka ku Etamu, nabwerera ku Pihahiroti, mzinda umene uli kuvuma kwa Baala-Zefoni. Ndipo adamanga mahema patsogolo pa Migidoli.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndipo atachoka ku Etamu, anabwerera ku Pihahiroti, kummawa kwa Baala-Zefoni, ndipo anamanga misasa yawo pafupi ndi Migidoli.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:7
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi kuti,


Lankhula ndi anthu a Israele, kuti abwerere m'mbuyo nagone patsogolo pa Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja, patsogolo pa Baala-Zefoni; pandunji pake mugone panyanja.


Ndipo Aejipito anawalondola, ndiwo akavalo ndi magaleta onse a Farao, ndi apakavalo ake, ndi nkhondo yake, nawapeza ali kuchigono kunyanja, pa Pihahiroti, patsogolo pa Baala-Zefoni.


Ndipo anachokera ku Pihahiroti, naoloka pakati pa nyanja nalowa m'chipululu; nayenda ulendo wa masiku atatu m'chipululu cha Etamu, namanga mu Mara.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa