Numeri 33:6 - Buku Lopatulika6 Nachokera ku Sukoti, nayenda namanga mu Etamu, ndiko ku malekezero a chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nachokera ku Sukoti, nayenda namanga m'Etamu, ndiko ku malekezero a chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adanyamuka ku Sukoti nakamanga mahema ku Etamu, mzinda umene uli m'mbali mwa chipululu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atachoka ku Sukoti anakamanga misasa yawo ku Etamu, mʼmbali mwa chipululu. Onani mutuwo |