Numeri 33:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo ana a Israele anachokera ku Ramsesi, nayenda namanga ku Sukoti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo ana a Israele anachokera ku Ramsesi, nayenda namanga ku Sukoti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pambuyo pake Aisraele adanyamuka ku Ramsesi nakamanga mahema ku Sukoti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Aisraeli atachoka ku Ramesesi, anamanga misasa yawo ku Sukoti. Onani mutuwo |