Numeri 33:4 - Buku Lopatulika4 pamene Aejipito analikuika oyamba kubadwa ao onse, amene Yehova adawakantha; Yehova adaweruzanso milungu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 pamene Aejipito analikuika oyamba kubadwa ao onse, amene Yehova adawakantha; Yehova adaweruzanso milungu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 M'menemo nkuti Aejipitowo akuika maliro a ana ao achisamba amene Chauta adaaŵapha pakati pao. Choncho Chauta adalipsira milungu ya Aejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 pamene ankayika maliro a ana awo oyamba kubadwa, omwe Yehova anawakantha pakati pawo chifukwa Yehova anaweruza milungu yawo. Onani mutuwo |