Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:49 - Buku Lopatulika

49 Ndipo anamanga pa Yordani, kuyambira ku Beteyesimoti kufikira ku Abele-Sitimu m'zidikha za Mowabu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 Ndipo anamanga pa Yordani, kuyambira ku Beteyesimoti kufikira ku Abele-Sitimu m'zidikha za Mowabu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 Adamanga mahema ao pafupi ndi mtsinje wa Yordani kuyambira ku Beteyesimoti mpaka ku Abele-Sitimu, m'zigwa za Mowabu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 Ali ku zigwa za Mowabu anamanga mʼmbali mwa Yorodani kuchokera ku Beti-Yesimoti mpaka ku Abeli-Sitimu.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:49
9 Mawu Ofanana  

Ndipo azipanga likasa la mtengo wakasiya: utali wake mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwake mkono ndi hafu, msinkhu wake mkono ndi hafu.


Ndipo uzipanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu.


ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;


chifukwa chake taona ndidzatsegula pambali pake pa Mowabu kuyambira kumizinda, kumizinda yake yokhala mphepete, yokometsetsa ya m'dziko, Beteyesimoti, Baala-Meoni, ndi Kiriyataimu,


Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'zigwa za Mowabu, tsidya la Yordani ku Yeriko.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko, nati,


ndi Betepeori, ndi matsikiro a Pisiga, ndi Beteyesimoti;


Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ali ku Sitimu, anatuma amuna awiri mosadziwika kukazonda, ndi kuti, Mukani, mulipenye dzikolo, ndi ku Yeriko. Ndipo anamuka nalowa m'nyumba ya mkazi wadama, dzina lake Rahabi, nagona momwemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa