Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 33:50 - Buku Lopatulika

50 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

50 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

50 Chauta adauza Mose m'zigwa za Mowabu pafupi ndi mtsinje wa Yordani, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

50 Pa zigwa za Mowabu, mʼmbali mwa Yorodani moyangʼanana ndi ku Yeriko, Yehova anawuza Mose kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:50
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'zigwa za Mowabu, tsidya la Yordani ku Yeriko.


Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mutaoloka Yordani kulowa m'dziko la Kanani,


Ndipo Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumu awa, ndi mafumu ao omwe nawakantha ndi lupanga lakuthwa, nawaononga konse; monga Mose mtumiki wa Yehova adalamulira.


Monga Yehova adalamulira Mose mtumiki wake, momwemo Mose analamulira Yoswa; momwemonso anachita Yoswa; sanachotsepo mau amodzi pa zonse Yehova adalamulira Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa