Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:48 - Buku Lopatulika

48 Nachokera ku mapiri a Abarimu, nayenda namanga m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 Nachokera ku mapiri a Abarimu, nayenda namanga m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Adanyamuka ku mapiri a Abarimu, nakamanga mahema ao ku zigwa za ku Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yordani ku Yeriko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 Atachoka ku mapiri a Abarimu anakamanga ku zigwa za Mowabu mʼmbali mwa Yorodani moyangʼanana ndi Yeriko.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:48
4 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'zigwa za Mowabu, tsidya la Yordani ku Yeriko.


Pamenepo Mose ndi Eleazara wansembe ananena nao m'zidikha za Mowabu pa Yordani kufupi ku Yeriko, ndi kuti,


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Kwera m'phiri ili la Abarimu, nupenye dziko limene ndapatsa ana a Israele.


natsika kuchokera ku Yanowa, kunka ku Ataroti, ndi ku Naara, nafika ku Yeriko, natuluka ku Yordani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa