Numeri 33:47 - Buku Lopatulika47 Nachokera ku Alimoni-Dibulataimu, nayenda namanga m'mapiri a Abarimu, chakuno cha Nebo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Nachokera ku Alimoni-Dibulataimu, nayenda namanga m'mapiri a Abarimu, chakuno cha Nebo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Adanyamuka ku Alimoni-dibulataimu, nakamanga mahema ao ku mapiri a Abarimu patsogolo pa Nebo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Atachoka ku Alimoni-Dibulataimu anakamanga mʼmapiri a Abarimu, pafupi ndi Nebo. Onani mutuwo |