Numeri 33:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo Mkanani, mfumu ya Aradi, wakukhala kumwera m'dziko la Kanani, anamva za kudza kwao kwa ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo Mkanani, mfumu ya Aradi, wakukhala kumwera m'dziko la Kanani, anamva za kudza kwao kwa ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Mfumu ya ku Aradi, Mkanani amene ankakhala m'dziko la Kanani, adamva kuti Aisraele akubwera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Mfumu ya Akanaani ya ku Aradi yomwe inkakhala ku Negevi kummwera kwa Kanaani, inamva kuti Aisraeli akubwera. Onani mutuwo |