Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:41 - Buku Lopatulika

41 Ndipo anachokera kuphiri la Hori, nayenda namanga mu Zalimona.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Ndipo anachokera kuphiri la Hori, nayenda namanga m'Zalimona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Pambuyo pake iwo adanyamuka ku phiri la Hori, nakamanga mahema ao ku Zalimona.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Atachoka ku phiri la Hori anakamanga ku Zalimoni.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:41
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anayenda ulendo kuchokera kuphiri la Hori, nadzera njira ya Nyanja Yofiira, kupaza ku dziko la Edomu; ndi mtima wa anthu unada chifukwa cha njirayo.


Ndipo Mkanani, mfumu ya Aradi, wakukhala kumwera m'dziko la Kanani, anamva za kudza kwao kwa ana a Israele.


Nachokera ku Zalimona, nayenda namanga mu Punoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa