Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:36 - Buku Lopatulika

36 Nachokera ku Eziyoni-Gebere, nayenda namanga m'chipululu cha Zini (ndiko Kadesi).

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Nachokera ku Eziyoni-Gebere, nayenda namanga m'chipululu cha Zini (ndiko Kadesi).

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Adanyamuka ku Eziyoni-Gebere, nakamanga mahema ao m'chipululu cha Zini (ndiye kuti Kadesi).

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Atachoka ku Ezioni-Geberi anakamanga ku Kadesi, mʼchipululu cha Zini chimene ndi Kadesi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:36
6 Mawu Ofanana  

Pamenepo anakwerako, nazonda dziko kuyambira chipululu za Zini kufikira Rehobu, polowa ku Hamati.


Ndipo anamuka, nadza kwa Mose, ndi Aroni, ndi khamu lonse la ana a Israele, ku chipululu cha Parani ku Kadesi; ndipo anabwezera mau iwowa, ndi khamu lonse, nawaonetsa zipatso za dzikoli.


Ndipo ana a Israele, ndilo khamu lonse, analowa m'chipululu cha Zini mwezi woyamba; ndipo anthu anakhala mu Kadesi; kumeneko anafa Miriyamu, naikidwa komweko.


popeza munapikisana nao mau anga m'chipululu cha Zini, potsutsana nane khamulo, osandipatula Ine pamadziwo pamaso pao. Ndiwo madzi a Meriba mu Kadesi, m'chipululu cha Zini.


Nachokera ku Aborona, nayenda namanga mu Eziyoni-Gebere.


popeza munandilakwira pakati pa ana a Israele ku madzi a Meriba wa Kadesi m'chipululu cha Zini, popeza simunandipatule Ine pakati pa ana a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa