Numeri 33:37 - Buku Lopatulika37 Nachokera ku Kadesi, nayenda namanga m'phiri la Hori, ku malekezero a dziko la Edomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Nachokera ku Kadesi, nayenda namanga m'phiri la Hori, ku malekezero a dziko la Edomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Adanyamuka ku Kadesi, nakamanga mahema ao ku phiri la Hori m'mbali mwa dziko la Edomu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Anachoka ku Kadesi ndi kukamanga ku phiri la Hori, mʼmalire mwa dziko la Edomu. Onani mutuwo |