Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 33:35 - Buku Lopatulika

35 Nachokera ku Aborona, nayenda namanga mu Eziyoni-Gebere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Nachokera ku Aborona, nayenda namanga m'Eziyoni-Gebere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Adanyamuka ku Aborona, nakamanga mahema ao ku Eziyoni-Gebere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Atachoka ku Abirona anakamanga ku Ezioni-Geberi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:35
7 Mawu Ofanana  

Yehosafati anamanga zombo za ku Tarisisi kukatenga golide ku Ofiri; koma sizinamuke, popeza zinaphwanyika pa Eziyoni-Gebere.


Ndipo mfumu Solomoni anamanga zombo zambiri ku Eziyoni-Gebere uli pafupi ndi Eloti, m'mphepete mwa Nyanja Yofiira, ku dziko la Edomu.


naphatikana naye kupanga zombo zomuka ku Tarisisi, nazipanga zombozo mu Eziyoni-Gebere.


Koma Aamaleke ndi Akanani akhala m'chigwamo; tembenukani mawa, nimunke ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.


Nachokera ku Yotibata, nayenda namanga mu Aborona.


Nachokera ku Eziyoni-Gebere, nayenda namanga m'chipululu cha Zini (ndiko Kadesi).


Potero tinapitirira abale athu, ana a Esau okhala mu Seiri, njira ya chidikha, ku Elati ndi ku Eziyoni-Gebere. Pamenepo tinatembenuka ndi kudzera njira ya chipululu cha Mowabu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa