Numeri 33:34 - Buku Lopatulika34 Nachokera ku Yotibata, nayenda namanga mu Aborona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Nachokera ku Yotibata, nayenda namanga m'Aborona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Adanyamuka ku Yotibata, nakamanga mahema ao ku Aborona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Atachoka ku Yotibata anakamanga ku Abirona. Onani mutuwo |