Numeri 33:33 - Buku Lopatulika33 Nachokera ku Hori Hagidigadi, nayenda namanga mu Yotibata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Nachokera ku Hori Hagidigadi, nayenda namanga m'Yotibata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Adanyamuka ku Horo-Hagidigadi, nakamanga mahema ao ku Yotibata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Atachoka ku Hori-Hagidigadi anakamanga ku Yotibata. Onani mutuwo |