Numeri 33:26 - Buku Lopatulika26 Nachokera ku Makeloti, nayenda namanga mu Tahata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Nachokera ku Makeloti, nayenda namanga m'Tahata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Adanyamuka ku Makeloti, nakamanga mahema ao ku Tahati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Atachoka ku Mekheloti anakamanga ku Tahati. Onani mutuwo |