Numeri 33:27 - Buku Lopatulika27 Nachokera ku Tahata, nayenda namanga mu Tera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Nachokera ku Tahata, nayenda namanga m'Tera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Adanyamuka ku Tahati, nakamanga mahema ao ku Tera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Atachoka ku Tahati anakamanga ku Tera. Onani mutuwo |