Numeri 33:25 - Buku Lopatulika25 Nachokera ku Harada, nayenda namanga mu Makeloti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Nachokera ku Harada, nayenda namanga m'Makeloti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Adanyamuka ku Harada, nakamanga mahema ao ku Makeloti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Atachoka ku Harada anakamanga ku Mekheloti. Onani mutuwo |