Numeri 33:24 - Buku Lopatulika24 Nachokera kuphiri la Sefera, nayenda namanga mu Harada. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Nachokera kuphiri la Sefera, nayenda namanga m'Harada. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Adanyamuka ku phiri la Sefera, nakamanga mahema ao ku Harada. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Atachoka ku phiri la Seferi anakamanga ku Harada. Onani mutuwo |