Numeri 33:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Mose analembera matulukidwe ao monga mwa maulendo ao, monga mwa mau a Yehova; ndipo maulendo ao ndi awa monga mwa matulukidwe ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Mose analembera matulukidwe ao monga mwa maulendo ao, monga mwa mau a Yehova; ndipo maulendo ao ndi awa monga mwa matulukidwe ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mose adalemba maina a malo onse oyambira ulendo ndi chigono chilichonse, monga Chauta adamlamula. Zigono zake potsata malo oyambira ulendo wao zinali motere: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mose analemba malo amene anayambira maulendo awo molamulidwa ndi Yehova. Maulendo awo ndi malo omwe anayambira ndi awa: Onani mutuwo |